Langwan Piksy - Tsoka Liyenda Lyrics
Kumbire adanka nawo
Palibe akanakhonza
Anasiya pa dzuwa anawo
Anayesa ndi malodza
Ankati satana
Wakhala pa nsana
Kuyamba kudana
Kufuna kuphana
Kuthana
Nzosauzana
Nthawi yakwana
Buluzi wa easy chitseko cha mpana
CHORUS
Anapita...
Langwan Piksy - Everyday Lyrics
Ati ndiri mchikondi... Well... that's obvious
Sikuti ndazelezeka... chikondi basi
Awesome palibe kutinamizayi
Made in heaven palibe kukakamiza ayi
I look at you and I sekelera
You complete me Kupanda iweyo I pelewera
Ukakhalapo n...
Langwan Piksy - Maloto Lyrics
VERSE 1
I saw mwana wanga
What a cute baby
Proud dad anzanga anamva mbebe
Kusiyana ndi ana ena iye anali star
Ndinagwada kuthokoza Mbuye wodalitsa
Tinapita tonse kukagula ma dyper
Titagwirana manja pamalo panaipa
Tinakula koma we we...