Mumbele Ndifuna Kudziwa Lyrics


Ndifuna Kudziwa by Mumbele

VERSE 1
Tawachititsa manyazi/
Ati chikondi chimakoma chikangoyamba/
Koma ife tachokea kutali/
Chimodzimodzi kukondana ngati poyamba/

Ti ma ex ndikumazachita nsanje/
Amayenda mbali amayesa masanje/
Pano mtima ndasiya mmanja mwako/
Ndipo chili chonse cha ine ndi chako, but forbid/

If I was tested like Job/
And I lost my property, money and job/
My balance is lost and my evens are odd/
And all but our love is left to fight the odds/

Girl would we survive? Would you remain by my side?
Would you be down for the ride and move with the tides?
Would your hands hold onto my heart?
If everything else fell apart?

CHORUS
Zikandivuta/
Ndikakanika/
Ndingadalile/
Pa iwe/

Popanda ndalama/
Popanda golide/
Chiondi cha ine/
Chingakukwanile/
Ndifuna kudziwa/

VERSE 2
Tawamvetsa kuwawa/
Zimatha kukhala chonchi chikondi anthu awili/
Eyetu, amachita kudabwa/
Ndipo omwe satidziwa anatimvela mbiri/

Power couple, here to cause trouble/
Hustlin' as one but success comes double/
Anthu nkumatisilila/
Nkumati zikubeba akawona zikuyenda, but forbid/

If I was tested like Job/
And I lost my property, money and job/
My balance is lost and my evens are odd/
And all but our love is left to fight the odds/

Will you understand? If there was no success at hand/
Will you still be the woman behind the man?
With no diamond ring to claim you as my bride/
Will you wear my heart with pride?

*CHORUS

Recently Searched Lyrics

Recently Viewed Lyrics